Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist

0

MWINI NDALAMA

Pa zinthu zomwe munthu amaganizira tsiku ndi tsiku ndalama  imakhala pa mndandanda wa zinthu zoganiziridwa. Kaganizidwe kangwiro nako ndi kofunikira pa nkhani ya ndalama. Benard  ChiluzI, yemwe ndi Mkulu oyang’ana za maphunziro abwino a kayendetsedwe ka chuma ,wati kuganiza molungama ndi kaganizidwe komwe sikungamupezetse munthu mavuto kapena ndi kuganiza mu njira ina chifukwa cha zinthu […]

HOT NEWS

0

LITSIRO LA MKATI MWA THUPI

Litsiro ndi chinthu chokhacho chimene tsiku lake lobadwa silimadziwika ndipo limaberekana mwa kathithi. Mthupi mwa munthu namo mumakhala litsiro. Namkungwi pa nkhani ya zakudya,  Gladys Bandawe ,kuchokera ku Hope nutrition Services, watutumutsa mtundu wa a Malawi ponena kuti mthupi mwa munthu mumakhala litsiro.” Mkati mwathupi mumakhala litsiro limene limafunika kutsuka chimodzimodzi   limene limakhala kunja kwa […]

0

M’KUSOKA ZOVALA MULI PHINDU

Pa miringo ya zinthu zomwe zimalingidwa pali mulingo umodzi wokha umene umapereka mafunso   ngati kalingidwe kakusemba ndondomeko maka olingayo akakhala wa mamuna ndipo akulinga munthu wa mkazi. Chovala , ndi chithu chokhacho chomwe chimalingidwa ndi mmisiri wosoka. Thomson Geza, Yemwe ndi mmodzi mwa wosoka zovala ku msika wa  Galliver mu mzinda wa Lilongwe, wavomereza kuti […]

0

MALAWI IKUFUNIKA MAPHUNZIRO A ZA CHUMA

Kusowa kwa maphunziro a za Chuma  pakati pa a Malawi  kuli ngati kusowa kwa  Chipatso cha Mpinjipinji Mnkhalango za dziko lino.Katswiri pa nkhani za Chuma a Innocent Banda, watsindika kuti ma Phunziro a za Chuma ndi osowa ngakhale ali ofunika. “Maphunziro a za chuma ndi ofunika chifukwa ndi chimene chimapereka mphamvu kwa anthu pothetsa umphawi,kutukula […]

0

BUNGWE LA ACB LIKUWODZERA

Ndizosabisa kunena kuti Moto wa khala la Mtengo wa Tsanya omwe umayaka ku Bungwe lothana ndi Katangale ndi Ziphuphu  tsopano uli ngati Moto wa Mapesi. Katswiri woyankhulapo pa nkhani za Utsogoleri wabwino komanso momwe zinthu zikuyendera mdziko muno   Victor  Chipofya, wati sakumva nkhani  mma Nyuzipepala  ngati momwe zinaliri mbuyomu .”Sitikumva zinthu mma Nyuzipepala ngati mmene […]

0

KAUNIUNI WA MOYO AZICHITIKA NDITHU PA MALAWI

Galimoto za mtidzi, nyumba za pamwamba  komanso zovala zodula  ndi zina mwa zinthu zomwe mtima umafuna utazipeza mmoyowu.Ichi chifukwa  chake pali mkuluwiko wotchedwa ‘mtima Suvala Sanza’. Davis Damison yemwe ndi mkulu wa Community Initiative for Social Empowerment (CISE)Malawi , wafotokoza kuti kauniuni wa Moyo (life style audit)ndi makhalidwe  a munthu potengera zinthu zimene wapeza kapena […]

0

MARY CHILIMA WAPEMPHA KAFUKUFUKU WAPADERA

Mdima wa ndiwe yani  wokhudza zomwe zidachitika kuti ndege yomwe idanyamula wachiwiri wa kale wa  Mtsogoleri wa dziko lino Malemu Dr Saulosi Klaus Chilima , udakakodolabe Mitsinje ya misonzi kwa a Mary Chilima ,omwe  pa 29 September 2024  adalemba pa tsamba la mchezo la facebook  kupempha  okhuzidwa onse kuti awathandize kupanga kafukufuku wapadera. Iwo adajambulitsa  […]

0

CHAKWERA WALAVULA MAKALA A MOTO KU UNGA

Mkuluwiko wokuti zingalume phula n’tenga ndi nkuluwiko omwe wamangirira  uthenga omwe Mtsogoleri wa dziko lino  Dr Lazalus Chakwera,  anali nawo kwa mamulumuzana a Bungwe la mgwirizano wa Maiko  apa dziko lonse lapansi. Mmodzi mwa akatswiri omwe amayankhulapo pa nkhani zosiyanasiyana mdziko muno a Dr George Chaima , ayamikira Mtsogoleri wa dziko lino  Dr Lazarus Chakwera […]

Take your favorite radio with you

Loading title
Loading artist

TODAY SHOWS

Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist