Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist

Blog one column

Page: 6

Malonda ambiri mdziko muno amayamba akwezedwa pa Sikelo asanasinthanitsidwe ndi ndalama. Ndi Malonda amodzi okha a Golide omwe atati akwezedwa pa Sikelo atha kusinthanitsidwa ndi 150 Million Malawi Kwacha pa Kilogram imodzi.Miyala ya Mtengo wapatali ndiyo ili ndi kuthekera koonjola anthu pa umphawi wa dzaoneni. Malingana ndi kafukufuku dziko la Malawi ndi dziko losaukitsitsa kwambiri […]

Tsiku silitha pasadachitike malonda aliwonse. A Zebron Lewis ochokera ku area 9 mu mzinda wa Lilongwe akhala akuchita geni. Bambo Lewis adayamba ndi geni yogulitsa Nyemba poyendanazo ku area 24, zaka zingapo zapitazo. Kuchulukana kwa anthu ogulitsa malondawa ku area 24,kudawapangitsa a Lewis kumakachitira geniyi ku area 25 ndi 49. Pakupita kwa nthawi nkuluyu adasintha […]


Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist