PHINDU LA MAPHUNZIRO A CHUMA KU MALAWI
Chuma ndi chinthu chimene chimafunikira kwambiri pa moyo wa munthu aliyense posatengera komwe munthu amachokera. Maphunziro a nkhani za chuma kuno kwathu ndi mnyanga wa njobvu. Katswiri pa nkhani ya zachuma,Innocent Banda watsindika kuti muli phindu mma phunziro a nkhani za chuma”Maphunziro a zachuma ali ndi phindu pa munthu payekha chifukwa Ndalama-zo amazipeza ndi munthu”. […]
KODI CHUMA CHA ZIPANI ZA NDALE CHIMA CHOKA KUTI?
Mawu akuti bongololo sadzolera mafuta pa gulu akugwirizana kwambiri ndi zomwe zipani za ndale zimachita pa nkhani youlula komwe kumachokera chuma chake. Victor Chipofya, yemwe ndi katswiri pa nkhani za ndale wati aMalawi samamvetsetsa momwe ndalama zoyendetsera zipani zimachokera.”Nthawi zambiri Chipani chokuti chiri kotsutsa chikangolowa m’boma chimayamba kugula magalimoto ankhaninkhani.Izi zimadabwitsa kuti ndalama azitenga kuti?.Nchifukwa […]
NYENGO YA MDZIKO LA MALAWI YASANDULIKA
Zovala zomwe anthu timavala zimagwirizana ndi nyengo, ntchito zathu zimene zimachitika malingana ndi Nyengo. Tikawunikira nyengo ya mvula kuno kwathu ku Malawi ,nayo idasintha. Chifundo Dalireni , yemwe ndi mmodzi mwa akatakwe a zachirengedwe watsimikiza kuti nyengo idasintha.”Nyengo idasintha pafupifupi pa dziko lonse lapansi”. Katswiriyu wafotokoza kuti kudula mitengo, kutulutsa utsi kwambiri ku ma fakitale […]
ZOYENERA KUCHITA PA MALO OGWIRA NTCHITO
Malo ogwirira ntchito ali ngati nyambo mmanja mwa mnsodzi ndipo kugwira ntchito kumayika chimwemwe mtsaya pomwe malipiro akuperekedwa.Komatu kuzindikira ntchito yako nkofunika pa Kampani kapena bungwe limene munthu akuligwirira ntchito. Mkulu ochokera ku Bungwe lolimbikitsa luso losiyanasiyana pakati pa achinyamata la CISE Malawi, a Davis Damison, wafotokoza kuti ndikofunikira kwambiri ngati bungwe kapena kampani kudziwa […]
MUNTHU SUTHYOVA NJINGA ULI PA MTSETSE
Mutha kuvomerezana nane kuti mwasiya kaye zimene mumachita ndipo mukuwerenga nkhani iyiyi. Mukamaliza, muzikonzekeretsa kuchita zinthu zina. Izi ndi chimodzimodzi ndi kuzikonzekeretsa mmoyo omwe mungakhale mutapuma pa ntchito kapena bizinezi. Benard Chiluzi, mphunzitsi wa kayendetsedwe kabwino ka chuma kuchokera ku old mutual, wadandaulira a Malawi kuti adzikhala akuikiza ndalama ngati njira imodzi yozikonzekeretsa kupuma pa […]
ZOYENERA KUCHITA PA MALO OGWIRA NTCHITO
Malo ogwirira ntchito ali ngati nyambo mmanja mwa mnsodzi ndipo kugwira ntchito kumayika chimwemwe mtsaya pomwe malipiro akuperekedwa.Komatu kuzindikira ntchito yako nkofunika pa Kampani kapena bungwe limene munthu akuligwirira ntchito. Mkulu ochokera ku Bungwe lolimbikitsa luso losiyanasiyana pakati pa achinyamata la CISE Malawi, a Davis Damison, wafotokoza kuti ndikofunikira kwambiri ngati bungwe kapena kampani kudziwa […]
Nyimbo ndi chinthu chokhacho chimene chimathuzitsa mtima pamene munthu ali m’chisoni, kukuza chimwemwe kwa munthu amene ali mchisangalalo komanso kuthandizira kugwira ntchito mosafooka. Gulu la Peace Soldiers , lomwe limayimba chamba cha Reggae, lati lidabadwa mu chaka cha 2003 ndi cholinga chofuna kupeza njira pa kulankhula pa zomwe gululi linkadana nazo ku Sukulu ya Secondary. […]
Pa zinthu zomwe munthu amaganizira tsiku ndi tsiku ndalama imakhala pa mndandanda wa zinthu zoganiziridwa. Kaganizidwe kangwiro nako ndi kofunikira pa nkhani ya ndalama. Benard ChiluzI, yemwe ndi Mkulu oyang’ana za maphunziro abwino a kayendetsedwe ka chuma ,wati kuganiza molungama ndi kaganizidwe komwe sikungamupezetse munthu mavuto kapena ndi kuganiza mu njira ina chifukwa cha zinthu […]