News
Page: 4
Boma la Malawi kudzera ku nthambi ya zachuma laonjola bank ya reserve ya mdziko mumo poipatsa ndalama zokwana 600 billion Malawi Kwacha kutsatira kuduka kwa bank yi ndi ndalama zokwana 539 billion Malawi. Katswiri pa nkhani zachuma a Greenson Nyirenda ,ati dziko lino siridafike pokhazikika pa chuma. Kuduka pa chuma kwa bank ya reserve kukutanthauza […]
Malonda ambiri mdziko muno amayamba akwezedwa pa Sikelo asanasinthanitsidwe ndi ndalama. Ndi Malonda amodzi okha a Golide omwe atati akwezedwa pa Sikelo atha kusinthanitsidwa ndi 150 Million Malawi Kwacha pa Kilogram imodzi.Miyala ya Mtengo wapatali ndiyo ili ndi kuthekera koonjola anthu pa umphawi wa dzaoneni. Malingana ndi kafukufuku dziko la Malawi ndi dziko losaukitsitsa kwambiri […]
Tsiku silitha pasadachitike malonda aliwonse. A Zebron Lewis ochokera ku area 9 mu mzinda wa Lilongwe akhala akuchita geni. Bambo Lewis adayamba ndi geni yogulitsa Nyemba poyendanazo ku area 24, zaka zingapo zapitazo. Kuchulukana kwa anthu ogulitsa malondawa ku area 24,kudawapangitsa a Lewis kumakachitira geniyi ku area 25 ndi 49. Pakupita kwa nthawi nkuluyu adasintha […]