Blog
Afreximbank reported strong financial performance despite a complex global economic landscape marked by geopolitical tensions, inflationary pressures, and elevated interest rate, posting a net income of US$973.5 million for FY 2024, a 29% increase from the previous year – with subsidiaries beginning to make meaningful contributions to the Group’s financial results. These impressive results highlight […]
The African Development Bank Group President, Dr. Akinwumi Adesina, has appointed the Right Honourable Andrew Mitchell as his Senior Advisor for resource mobilization and policy issues on a pro bono basis. Rt. Hon. Mitchell, whose appointment is effective 7 April 2025, will provide strategic advice on emerging global and regional development issues and high-level political […]
Striving to increase production and reverse natural declines in mature oilfields, Ghana is promoting new investment across its upstream oil and gas sector. The country – through national upstream regulator the Petroleum Commission of Ghana – is embarking on a series of industry reforms that aim to strengthen the operating environment for oil and gas […]
The escalation of violent conflict in recent months has pushed hundreds of thousands of people in eastern Democratic Republic of Congo (DRC) into desperate conditions, warns the Norwegian Refugee Council (NRC) Secretary General Jan Egeland on a visit this week. Displaced families sheltering at temporary sites have once again been forced to flee, as fighting […]
Nzosakaikitsa kuti mphindi zingapo zapitazi mwangomaliza kumene kudya chakudya, ndipo mukatha kuwerenga nkhani-yi sizikhala zachilendo kuti Njala ikuimbirani likhweru kuti mudye chakudya chinachake.Koma nkhani yagona pa chakudya choyenera mthupi la munthu. Naomi Mvula, yemwe ndi katswiiri wotsatira kadyedwe ka bwino,watambasula za chakudya chabwino. “Pali zakudya ma gulu asanu ndi limodzi .Zakudya zokhutitsa ; Chinangwa, Mbatata, […]
Ngati muli pa Msika, tasuzumirani kumalo ogulitsira nyama kuphatikizapo nyama ya nkhuku. Mugwirizana nane kuti ndiwo ya nyama, ndiyokhayo yomwe imapangitsa phwando kapena mwambo wa Maliro kukhala osimbika. Nthawi zinanso angakhale ku Chilendo kumene akakuphikira nyama, umakhala ndi chimwemwe chodzala mtsaya. A James Simika ,omwe ndi mmodzi mwa anthu ochita Malonda ogulitsa nyama akusimba za […]
Nyimbo ndi chinthu chimodzi chimene chimapezeka mnyengo zonse za munthu. Mkulu wa bungwe loyanga’anira oyimba mdziko muno la Musicians Union of Malawi ,Vita Chirwa, akufotokoza za momwe mayimbidwe akuyendera. “Maimbidwe kuno kwathu ku Malawi, akupita patsogolo. Taona oyimba kuno kwathu akuitanidwa kupita kukayimba ku Mayiko akunja komanso kuwina photho za padziko lonse”. Vita wayamikira atsogoleri […]
Pamene mumatsegula tsambali kuti muwerenge nkhaniyi ,ndiri nacho chikhulupiriro kuti munakonzekera.Munthu umakhala kakasi kapena kusowa mtengo ogwira ngati sunakonzekere pakuchita chinachake.Mbusa Vincent Nguluwe, watambasula kukonzekera kuti ndi kukonzekera zinthu zomwe munthu ukufuna kuti uchite kuti ukafikire china chake. “Kukonzikera kudayamba ndi Mulungu. Genesis 1 ndime ya 1″. Watero , Nguluwe. Mbusayu, wati kukonzekera kumathandizira munthu […]
Zolemba zambiri zimafotokoza kuti ulimi ndi kudzala mbewu komanso kuweta zifuyo pa Malo ogwiritsidwa ntchito ndi anthu. Mutha kututumuka mutamva kuti ulimi ndi kudzala mbewu, kuweta Nyama ndi kubzala mitengo, pozisamalira ndi kuikolola. Musatutumuke ndi zomwe mwamvazi popeza izi ndi zochitika ndithu. Mkulu wa kampani ya Headman Nursery , Elijah Nyirenda ochokera ku Nkhatabay, wafotokoza […]
Chuma ndi chinthu chimene chimafunikira kwambiri pa moyo wa munthu aliyense posatengera komwe munthu amachokera. Maphunziro a nkhani za chuma kuno kwathu ndi mnyanga wa njobvu. Katswiri pa nkhani ya zachuma,Innocent Banda watsindika kuti muli phindu mma phunziro a nkhani za chuma”Maphunziro a zachuma ali ndi phindu pa munthu payekha chifukwa Ndalama-zo amazipeza ndi munthu”. […]