Kasupe News
Page: 2
Pa miringo ya zinthu zomwe zimalingidwa pali mulingo umodzi wokha umene umapereka mafunso ngati kalingidwe kakusemba ndondomeko maka olingayo akakhala wa mamuna ndipo akulinga munthu wa mkazi. Chovala , ndi chithu chokhacho chomwe chimalingidwa ndi mmisiri wosoka. Thomson Geza, Yemwe ndi mmodzi mwa wosoka zovala ku msika wa Galliver mu mzinda wa Lilongwe, wavomereza kuti […]
Kusowa kwa maphunziro a za Chuma pakati pa a Malawi kuli ngati kusowa kwa Chipatso cha Mpinjipinji Mnkhalango za dziko lino.Katswiri pa nkhani za Chuma a Innocent Banda, watsindika kuti ma Phunziro a za Chuma ndi osowa ngakhale ali ofunika. “Maphunziro a za chuma ndi ofunika chifukwa ndi chimene chimapereka mphamvu kwa anthu pothetsa umphawi,kutukula […]
Ndizosabisa kunena kuti Moto wa khala la Mtengo wa Tsanya omwe umayaka ku Bungwe lothana ndi Katangale ndi Ziphuphu tsopano uli ngati Moto wa Mapesi. Katswiri woyankhulapo pa nkhani za Utsogoleri wabwino komanso momwe zinthu zikuyendera mdziko muno Victor Chipofya, wati sakumva nkhani mma Nyuzipepala ngati momwe zinaliri mbuyomu .”Sitikumva zinthu mma Nyuzipepala ngati mmene […]
Mdima wa ndiwe yani wokhudza zomwe zidachitika kuti ndege yomwe idanyamula wachiwiri wa kale wa Mtsogoleri wa dziko lino Malemu Dr Saulosi Klaus Chilima , udakakodolabe Mitsinje ya misonzi kwa a Mary Chilima ,omwe pa 29 September 2024 adalemba pa tsamba la mchezo la facebook kupempha okhuzidwa onse kuti awathandize kupanga kafukufuku wapadera. Iwo adajambulitsa […]
Mkuluwiko wokuti zingalume phula n’tenga ndi nkuluwiko omwe wamangirira uthenga omwe Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazalus Chakwera, anali nawo kwa mamulumuzana a Bungwe la mgwirizano wa Maiko apa dziko lonse lapansi. Mmodzi mwa akatswiri omwe amayankhulapo pa nkhani zosiyanasiyana mdziko muno a Dr George Chaima , ayamikira Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera […]
A baseline survey conducted by RBM in 2014 revealed that only 17% of adults utilized formal financial services, while a significant 53% relied on informal options. This gap is largely attributed to a lack of understanding of formal financial products, reflected in a concerning financial literacy index of just 3.6%. RBM Governor Wilson Banda emphasized […]
Sabata silimatha anthu okhala Mmizinda ndi mma town a Dziko lino asadaone zibinyira za zinyalala mphepete mwa Misewu zikudikira kunyamulidwa kuti zipite ku Mtaya. A Stephen Chiunjira ndi nkulu wa Bungwe la Our World international ,yomwe imapanga zosintha zinyalala kuti zikhale Manyowa ndi zinthu zina zosiyanasiyana ku Kawale 2, mu Mzinda wa Lilongwe . Iwo […]
Kwa nthawi yaitali anthu mdziko muno akhala akututumuka ndi imfa zokudza pongodzipha.A Joseph Maseke, katswiri pa nkhani yoona za thanzi la mmalingaliro watambasula kuti kaganizidwe ka ngwiro ndi kukhala osakhumudwa kapena nkhawa mmalingaliro. A Maseke atchula ma ubwenzi amene achinyamata amakhala nawo kuti ali ndi kuthekera kwa kukulu kokhudza kaganizidwe ka ngwiro. Katswiri-yu wadandaula kuti […]
Munthu umafika ponyasitsa nkhope pamene maso ako akumanizana ndi zinyalala mmizinda ndi mma town a dziko lino.Bungwe la Clean Cities Project lidabadwa ndi cholinga chofuna kulimbikitsa kusamalira chirengedwe, kusintha kwa Nyengo ndi ukhondo. Mtsogoleri wa Bungwe-li, Martin Manyozo wati iwo monga achinyamata ndi anthu okonda dziko lino kotero kuti akufuna kuthandizira kusintha mizinda yathu malingana […]
Recent developments in Malawi’s efforts to combat hunger have sparked a range of reactions from agricultural experts, Members of Parliament, and other stakeholders. The government’s announcement of maize distribution has become a contentious issue, with varying opinions on the fairness and effectiveness of the allocation of maize. Minister of Agriculture, Sam Kawale recently revealed in […]