Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist

0

MPHAMVU YA NYIMBO ZÀ KU MALAWI

Nyimbo ndi chinthu chimodzi chimene chimapezeka mnyengo zonse  za munthu. Mkulu wa bungwe loyanga’anira oyimba mdziko muno la Musicians  Union of Malawi ,Vita  Chirwa, akufotokoza za momwe mayimbidwe akuyendera. “Maimbidwe kuno  kwathu  ku Malawi, akupita patsogolo. Taona oyimba  kuno kwathu akuitanidwa kupita kukayimba ku Mayiko akunja komanso kuwina photho za padziko lonse”. Vita wayamikira atsogoleri  […]

0

UBWINO WA KUKONZEKERA POCHITA ZINTHU.

Pamene mumatsegula tsambali kuti muwerenge nkhaniyi ,ndiri nacho chikhulupiriro  kuti munakonzekera.Munthu umakhala kakasi kapena kusowa mtengo ogwira ngati  sunakonzekere pakuchita chinachake.Mbusa Vincent  Nguluwe, watambasula kukonzekera kuti ndi kukonzekera zinthu zomwe munthu ukufuna kuti uchite kuti ukafikire china chake. “Kukonzikera kudayamba ndi Mulungu. Genesis 1 ndime ya 1″. Watero , Nguluwe.  Mbusayu, wati kukonzekera kumathandizira munthu […]

0

CHIMWEMWE MU ULIMI WA MITENGO

Zolemba zambiri  zimafotokoza kuti ulimi ndi kudzala mbewu komanso kuweta zifuyo pa Malo ogwiritsidwa ntchito ndi anthu. Mutha kututumuka mutamva kuti ulimi  ndi kudzala mbewu, kuweta Nyama ndi kubzala mitengo, pozisamalira ndi kuikolola. Musatutumuke ndi zomwe mwamvazi popeza izi ndi zochitika ndithu. Mkulu wa  kampani ya Headman Nursery , Elijah Nyirenda ochokera ku Nkhatabay, wafotokoza […]

0

PHINDU LA MAPHUNZIRO A CHUMA KU MALAWI

Chuma ndi chinthu chimene chimafunikira kwambiri pa moyo wa munthu aliyense posatengera komwe  munthu amachokera. Maphunziro a nkhani za chuma kuno kwathu ndi mnyanga wa njobvu. Katswiri pa nkhani ya zachuma,Innocent Banda watsindika kuti  muli phindu mma phunziro a nkhani za chuma”Maphunziro a zachuma ali ndi  phindu pa munthu payekha chifukwa Ndalama-zo amazipeza ndi munthu”. […]

0

KODI CHUMA CHA ZIPANI ZA NDALE CHIMA CHOKA KUTI?

Mawu akuti bongololo sadzolera mafuta pa gulu akugwirizana kwambiri ndi zomwe zipani za ndale zimachita pa nkhani youlula komwe kumachokera chuma chake. Victor Chipofya, yemwe ndi katswiri pa nkhani za ndale wati  aMalawi samamvetsetsa momwe ndalama zoyendetsera zipani zimachokera.”Nthawi zambiri Chipani chokuti chiri kotsutsa chikangolowa m’boma chimayamba kugula magalimoto ankhaninkhani.Izi zimadabwitsa kuti ndalama azitenga kuti?.Nchifukwa […]

0

PHINDU LA MAPHUNZIRO A CHUMA KU MALAWI

Chuma ndi chinthu chimene chimafunikira kwambiri pa moyo wa munthu aliyense posatengera komwe  munthu amachokera. Maphunziro a nkhani za chuma kuno kwathu ndi mnyanga wa njobvu. Katswiri pa nkhani ya zachuma,Innocent Banda watsindika kuti  muli phindu mma phunziro a nkhani za chuma”Maphunziro a zachuma ali ndi  phindu pa munthu payekha chifukwa Ndalama-zo amazipeza ndi munthu”. […]

Mutha kuvomerezana nane kuti  mwasiya kaye zimene mumachita ndipo mukuwerenga nkhani iyiyi. Mukamaliza, muzikonzekeretsa kuchita zinthu zina. Izi ndi chimodzimodzi ndi kuzikonzekeretsa mmoyo omwe mungakhale mutapuma pa ntchito kapena  bizinezi. Benard Chiluzi, mphunzitsi wa kayendetsedwe kabwino ka chuma  kuchokera ku old mutual, wadandaulira a Malawi  kuti adzikhala akuikiza ndalama  ngati njira imodzi  yozikonzekeretsa kupuma pa […]

Zamoyo zirizonse zimayenera kulandira chakudya cha bwino  kuti zidzikula ndi thanzi. Nayo mbewu ndi chimodzi mwa zinthu za Moyo zomwe zimafuna zakudya zabwino.A Tyson Chapuma, yemwe ndi Mlangizi pa nkhani za Ulimi ku Lunyangwa  research station  m’boma la Mzuzu , wati akugwira ntchito  usiku ndi usana kufufuza za chakudya cha mbewu mu nthaka. Pothirirapo mulomo […]

Kasupe Radio Live

Kasupe Radio Live

Current track

Title

Artist